×

Ndipo Ife tidakhazikitsa mapiri pa dziko lapansi molimba kuti asagwedezeke pamodzi ndi 21:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:31) ayat 31 in Chichewa

21:31 Surah Al-Anbiya’ ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 31 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿وَجَعَلۡنَا فِي ٱلۡأَرۡضِ رَوَٰسِيَ أَن تَمِيدَ بِهِمۡ وَجَعَلۡنَا فِيهَا فِجَاجٗا سُبُلٗا لَّعَلَّهُمۡ يَهۡتَدُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 31]

Ndipo Ife tidakhazikitsa mapiri pa dziko lapansi molimba kuti asagwedezeke pamodzi ndi iwo ndipo tidakhazikitsa misewu pa miyala kuti mwina atsogozedwe

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وجعلنا في الأرض رواسي أن تميد بهم وجعلنا فيها فجاجا سبلا لعلهم, باللغة نيانجا

﴿وجعلنا في الأرض رواسي أن تميد بهم وجعلنا فيها فجاجا سبلا لعلهم﴾ [الأنبيَاء: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tidaika mapiri panthaka molimbika kuti isagwedezeke ndi iwo, ndipo m’menemo tidaikamo misewu kuti alondole njira (ndikufika komwe afuna)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek