×

Ndithudi Atumwi ena, adachitidwa chipongwe kale, koma anthu a chipongwe adafafanizidwa ndi 21:41 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:41) ayat 41 in Chichewa

21:41 Surah Al-Anbiya’ ayat 41 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 41 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿وَلَقَدِ ٱسۡتُهۡزِئَ بِرُسُلٖ مِّن قَبۡلِكَ فَحَاقَ بِٱلَّذِينَ سَخِرُواْ مِنۡهُم مَّا كَانُواْ بِهِۦ يَسۡتَهۡزِءُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 41]

Ndithudi Atumwi ena, adachitidwa chipongwe kale, koma anthu a chipongwe adafafanizidwa ndi chilango chimene iwo adachichitira chipongwe

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد استهزئ برسل من قبلك فحاق بالذين سخروا منهم ما كانوا به, باللغة نيانجا

﴿ولقد استهزئ برسل من قبلك فحاق بالذين سخروا منهم ما كانوا به﴾ [الأنبيَاء: 41]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ndithu atumiki adachitidwa chipongwe patsogolo pako; choncho amene adachita chipongwe mwa iwo, zidawadzera zomwe adali kuzichita chipongwe
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek