Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 63 - الأنبيَاء - Page - Juz 17
﴿قَالَ بَلۡ فَعَلَهُۥ كَبِيرُهُمۡ هَٰذَا فَسۡـَٔلُوهُمۡ إِن كَانُواْ يَنطِقُونَ ﴾
[الأنبيَاء: 63]
﴿قال بل فعله كبيرهم هذا فاسألوهم إن كانوا ينطقون﴾ [الأنبيَاء: 63]
Khaled Ibrahim Betala “(Iye) adati: “(Iyayi), koma wachita ichi ndi mkulu wawoyu. Choncho afunseni (kuti akuuzeni zenizeni) ngati amatha kuyankhula.” |