×

Ndi Zakariya pamene anaitana Ambuye wake nati, “Ambuye wanga! Musandileke ndekha. Ndipo 21:89 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Anbiya’ ⮕ (21:89) ayat 89 in Chichewa

21:89 Surah Al-Anbiya’ ayat 89 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Anbiya’ ayat 89 - الأنبيَاء - Page - Juz 17

﴿وَزَكَرِيَّآ إِذۡ نَادَىٰ رَبَّهُۥ رَبِّ لَا تَذَرۡنِي فَرۡدٗا وَأَنتَ خَيۡرُ ٱلۡوَٰرِثِينَ ﴾
[الأنبيَاء: 89]

Ndi Zakariya pamene anaitana Ambuye wake nati, “Ambuye wanga! Musandileke ndekha. Ndipo Inu ndinu wabwinomwaokhalitsaonse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وزكريا إذ نادى ربه رب لا تذرني فردا وأنت خير الوارثين, باللغة نيانجا

﴿وزكريا إذ نادى ربه رب لا تذرني فردا وأنت خير الوارثين﴾ [الأنبيَاء: 89]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (akumbutse za) Zakariya pamene adaitana Mbuye wake (kuti): “Mbuye wanga! Musandisiye ndekha; ndithu Inu ndinu wabwino kuposa alowa mmalo onse.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek