Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 27 - الحج - Page - Juz 17
﴿وَأَذِّن فِي ٱلنَّاسِ بِٱلۡحَجِّ يَأۡتُوكَ رِجَالٗا وَعَلَىٰ كُلِّ ضَامِرٖ يَأۡتِينَ مِن كُلِّ فَجٍّ عَمِيقٖ ﴾
[الحج: 27]
﴿وأذن في الناس بالحج يأتوك رجالا وعلى كل ضامر يأتين من كل﴾ [الحج: 27]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo (tidamuuza): “Lengeza kwa anthu za Hajj; akudzera (ena) oyenda ndi mapazi, ndipo (ena ali) pamwamba pa chiweto choonda (chifukwa chamasautso a paulendo); adza kuchokera kunjira zamtalimtali |