×

Musapembedze wina aliyense koma Mulungu ndipo musatumikire milungu ina. Aliyense amene amatumikira 22:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hajj ⮕ (22:31) ayat 31 in Chichewa

22:31 Surah Al-hajj ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 31 - الحج - Page - Juz 17

﴿حُنَفَآءَ لِلَّهِ غَيۡرَ مُشۡرِكِينَ بِهِۦۚ وَمَن يُشۡرِكۡ بِٱللَّهِ فَكَأَنَّمَا خَرَّ مِنَ ٱلسَّمَآءِ فَتَخۡطَفُهُ ٱلطَّيۡرُ أَوۡ تَهۡوِي بِهِ ٱلرِّيحُ فِي مَكَانٖ سَحِيقٖ ﴾
[الحج: 31]

Musapembedze wina aliyense koma Mulungu ndipo musatumikire milungu ina. Aliyense amene amatumikira milungu ina yoonjezera pa Mulungu weniweni, ali ngati iye amene agwa kuchokera kumwamba, ndipo asanagwe pansi, amalandiridwa ndi mbalame kapena kunyamulidwa ndi mphepo kukam’taya kumalo akutali

❮ Previous Next ❯

ترجمة: حنفاء لله غير مشركين به ومن يشرك بالله فكأنما خر من السماء, باللغة نيانجا

﴿حنفاء لله غير مشركين به ومن يشرك بالله فكأنما خر من السماء﴾ [الحج: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Uku mutapendekera kwa Allah Yekha, osati kum’phatikiza (Allah). Ndipo amene akuphatikiza Allah ndi mafano, ali ngati wogwa kuchokera kumwamba, kenako mbalame nkumuwakha, kapena mphepo kukamtaya malo akutali
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek