×

Kodi iwe siudziwa kuti Mulungu amadziwa zonse zimene zili kumwamba ndi pa 22:70 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hajj ⮕ (22:70) ayat 70 in Chichewa

22:70 Surah Al-hajj ayat 70 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 70 - الحج - Page - Juz 17

﴿أَلَمۡ تَعۡلَمۡ أَنَّ ٱللَّهَ يَعۡلَمُ مَا فِي ٱلسَّمَآءِ وَٱلۡأَرۡضِۚ إِنَّ ذَٰلِكَ فِي كِتَٰبٍۚ إِنَّ ذَٰلِكَ عَلَى ٱللَّهِ يَسِيرٞ ﴾
[الحج: 70]

Kodi iwe siudziwa kuti Mulungu amadziwa zonse zimene zili kumwamba ndi pa dziko lapansi? Ndithudi zonse zidalembedwa m’Buku lake. Ndithudi zimenezo ndi zosavuta kwa Mulungu

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم تعلم أن الله يعلم ما في السماء والأرض إن ذلك في, باللغة نيانجا

﴿ألم تعلم أن الله يعلم ما في السماء والأرض إن ذلك في﴾ [الحج: 70]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi sudziwa kuti Allah akudziwa zakumwamba ndi zapansi? Ndithu zonsezo zili m’kaundula (Wake), ndithu (kudziwika kwa) zimenezo kwa Allah nzosavuta
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek