×

Ndipo iwo ali kupembedza zinthu zina mowonjezera pa Mulungu, zinthu zimene sanapatsidwe 22:71 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-hajj ⮕ (22:71) ayat 71 in Chichewa

22:71 Surah Al-hajj ayat 71 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-hajj ayat 71 - الحج - Page - Juz 17

﴿وَيَعۡبُدُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ مَا لَمۡ يُنَزِّلۡ بِهِۦ سُلۡطَٰنٗا وَمَا لَيۡسَ لَهُم بِهِۦ عِلۡمٞۗ وَمَا لِلظَّٰلِمِينَ مِن نَّصِيرٖ ﴾
[الحج: 71]

Ndipo iwo ali kupembedza zinthu zina mowonjezera pa Mulungu, zinthu zimene sanapatsidwe umboni kuti azizigwadira ndipo ndi zimene iwo salikuzindikira. Ndithudi, anthu ochimwa alibe wowathandiza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ويعبدون من دون الله ما لم ينـزل به سلطانا وما ليس لهم, باللغة نيانجا

﴿ويعبدون من دون الله ما لم ينـزل به سلطانا وما ليس لهم﴾ [الحج: 71]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akupembedza milungu yabodza, kusiya Allah, yomwe (Allah) sadaitumizire umboni wakuti (ipembedzedwe) yomwenso iwo sakuidziwa bwino. Ndipo anthu osalungama sadzakhala ndi owathandiza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek