Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 11 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿ٱلَّذِينَ يَرِثُونَ ٱلۡفِرۡدَوۡسَ هُمۡ فِيهَا خَٰلِدُونَ ﴾
[المؤمنُون: 11]
﴿الذين يرثون الفردوس هم فيها خالدون﴾ [المؤمنُون: 11]
Khaled Ibrahim Betala “Amene adzalandira Munda wamtendere (wotchedwa) Fir’dausi (Munda wapamwamba kwambiri). M’menemo iwo adzakhala nthawi yaitali |