×

Ife timatumiza madzi kuchokera kumwamba m’muyeso wokwana ndipo timawalowetsa pansi pa nthaka. 23:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mu’minun ⮕ (23:18) ayat 18 in Chichewa

23:18 Surah Al-Mu’minun ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 18 - المؤمنُون - Page - Juz 18

﴿وَأَنزَلۡنَا مِنَ ٱلسَّمَآءِ مَآءَۢ بِقَدَرٖ فَأَسۡكَنَّٰهُ فِي ٱلۡأَرۡضِۖ وَإِنَّا عَلَىٰ ذَهَابِۭ بِهِۦ لَقَٰدِرُونَ ﴾
[المؤمنُون: 18]

Ife timatumiza madzi kuchokera kumwamba m’muyeso wokwana ndipo timawalowetsa pansi pa nthaka. Ndipo Ife tili ndi mphamvu yowachotsa madziwo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وأنـزلنا من السماء ماء بقدر فأسكناه في الأرض وإنا على ذهاب به, باللغة نيانجا

﴿وأنـزلنا من السماء ماء بقدر فأسكناه في الأرض وإنا على ذهاب به﴾ [المؤمنُون: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tatsitsa madzi mwamuyeso kuchokera kumwamba, ndi kuwakhazikitsa m’nthaka; ndipo ndithu Ife ndi okhoza kuwachotsa (kuti musathandizike nawo, koma sitidachite zimenezo chifukwa chokuchitirani chifundo)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek