×

Ndipo nena: “Ambuye wanga! Ndithandizeni kuti ndikafike pamalo podalitsika chifukwa Inu ndinu 23:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Mu’minun ⮕ (23:29) ayat 29 in Chichewa

23:29 Surah Al-Mu’minun ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 29 - المؤمنُون - Page - Juz 18

﴿وَقُل رَّبِّ أَنزِلۡنِي مُنزَلٗا مُّبَارَكٗا وَأَنتَ خَيۡرُ ٱلۡمُنزِلِينَ ﴾
[المؤمنُون: 29]

Ndipo nena: “Ambuye wanga! Ndithandizeni kuti ndikafike pamalo podalitsika chifukwa Inu ndinu wabwino wa onse amene amafikitsa pamalo okocheza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقل رب أنـزلني منـزلا مباركا وأنت خير المنـزلين, باللغة نيانجا

﴿وقل رب أنـزلني منـزلا مباركا وأنت خير المنـزلين﴾ [المؤمنُون: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo (potsika), nena: “E Mbuye wanga! Nditsitseni; kutsitsa kwa madalitso, pakuti Inu ndinu wotsitsa bwino kwambiri kuposa otsitsa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek