Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 30 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَٰتٖ وَإِن كُنَّا لَمُبۡتَلِينَ ﴾
[المؤمنُون: 30]
﴿إن في ذلك لآيات وإن كنا لمبتلين﴾ [المؤمنُون: 30]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu m’zimenezi muli zisonyezo. Ndithu Ife tili (ndi udindo) wowayesa ndi mayeso osiyanasiyana |