Quran with Chichewa translation - Surah Al-Mu’minun ayat 72 - المؤمنُون - Page - Juz 18
﴿أَمۡ تَسۡـَٔلُهُمۡ خَرۡجٗا فَخَرَاجُ رَبِّكَ خَيۡرٞۖ وَهُوَ خَيۡرُ ٱلرَّٰزِقِينَ ﴾
[المؤمنُون: 72]
﴿أم تسألهم خرجا فخراج ربك خير وهو خير الرازقين﴾ [المؤمنُون: 72]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi kapena ukuwapempha malipiro (nchifukwa chake akuchikana chipembedzochi)? Koma malipiro a Mbuye wako ndiwo abwino; ndipo Iye ndi Wopereka Wabwino kuposa opereka |