×

Iwo amene amanamizira akazi odzisunga kuti achita chigololo ndipo sangathe kutulutsa mboni 24:4 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:4) ayat 4 in Chichewa

24:4 Surah An-Nur ayat 4 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 4 - النور - Page - Juz 18

﴿وَٱلَّذِينَ يَرۡمُونَ ٱلۡمُحۡصَنَٰتِ ثُمَّ لَمۡ يَأۡتُواْ بِأَرۡبَعَةِ شُهَدَآءَ فَٱجۡلِدُوهُمۡ ثَمَٰنِينَ جَلۡدَةٗ وَلَا تَقۡبَلُواْ لَهُمۡ شَهَٰدَةً أَبَدٗاۚ وَأُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡفَٰسِقُونَ ﴾
[النور: 4]

Iwo amene amanamizira akazi odzisunga kuti achita chigololo ndipo sangathe kutulutsa mboni zinayi, akwapulidwe zikoti makumi asanu ndi atatu. Mukane umboni wawo mpaka kalekale. Anthu otere ndi oononga

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين يرمون المحصنات ثم لم يأتوا بأربعة شهداء فاجلدوهم ثمانين جلدة ولا, باللغة نيانجا

﴿والذين يرمون المحصنات ثم لم يأتوا بأربعة شهداء فاجلدوهم ثمانين جلدة ولا﴾ [النور: 4]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akunamizira akazi odziteteza (powanamizira kuti achita chiwerewere), ndipo osabwera nazo mboni zinayi, akwapuleni zikoti ; ndiponso musauvomereze umboni wawo mpaka kalekale. Iwo ngotuluka m’chilamulo cha Allah
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek