Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 44 - النور - Page - Juz 18
﴿يُقَلِّبُ ٱللَّهُ ٱلَّيۡلَ وَٱلنَّهَارَۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَعِبۡرَةٗ لِّأُوْلِي ٱلۡأَبۡصَٰرِ ﴾
[النور: 44]
﴿يقلب الله الليل والنهار إن في ذلك لعبرة لأولي الأبصار﴾ [النور: 44]
Khaled Ibrahim Betala “Allah amasintha usiku ndi usana (pambuyo pa usiku, umadza usana, ndipo pambuyo pa usana, umadza usiku). Ndithu m’zimenezo muli phunziro kwa anthu ozindikira (zinthu) |