×

Ndithudi tawatumizira pakati pawo, kuti akhoza kukumbukira, chisomo cha Mulungu koma anthu 25:50 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:50) ayat 50 in Chichewa

25:50 Surah Al-Furqan ayat 50 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 50 - الفُرقَان - Page - Juz 19

﴿وَلَقَدۡ صَرَّفۡنَٰهُ بَيۡنَهُمۡ لِيَذَّكَّرُواْ فَأَبَىٰٓ أَكۡثَرُ ٱلنَّاسِ إِلَّا كُفُورٗا ﴾
[الفُرقَان: 50]

Ndithudi tawatumizira pakati pawo, kuti akhoza kukumbukira, chisomo cha Mulungu koma anthu ambiri amakana. Ndipo iwo amasankha kusakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولقد صرفناه بينهم ليذكروا فأبى أكثر الناس إلا كفورا, باللغة نيانجا

﴿ولقد صرفناه بينهم ليذكروا فأبى أكثر الناس إلا كفورا﴾ [الفُرقَان: 50]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndiponso ndithu tikuigawa (mvulayi) pakati pawo kuti akumbukire, ndipo anthu ambiri akukana (kuthokoza Allah) koma kupitiriza kusakhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek