Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 4 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿إِن نَّشَأۡ نُنَزِّلۡ عَلَيۡهِم مِّنَ ٱلسَّمَآءِ ءَايَةٗ فَظَلَّتۡ أَعۡنَٰقُهُمۡ لَهَا خَٰضِعِينَ ﴾
[الشعراء: 4]
﴿إن نشأ ننـزل عليهم من السماء آية فظلت أعناقهم لها خاضعين﴾ [الشعراء: 4]
Khaled Ibrahim Betala “Tikadafuna, tikadawatsitsira chizizwa kuchokera kumwamba; kotero kuti makosi awo akadadzichepetsa ndi chizizwacho, (sakadatha kucheukira kwina koma sitifuna kukakamiza anthu kuti akhale Asilamu) |