×

Mitima yawo idadziwa kuti zizindikiro zidali zoona koma adazikana izo chifukwa chakulakwa 27:14 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Naml ⮕ (27:14) ayat 14 in Chichewa

27:14 Surah An-Naml ayat 14 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 14 - النَّمل - Page - Juz 19

﴿وَجَحَدُواْ بِهَا وَٱسۡتَيۡقَنَتۡهَآ أَنفُسُهُمۡ ظُلۡمٗا وَعُلُوّٗاۚ فَٱنظُرۡ كَيۡفَ كَانَ عَٰقِبَةُ ٱلۡمُفۡسِدِينَ ﴾
[النَّمل: 14]

Mitima yawo idadziwa kuti zizindikiro zidali zoona koma adazikana izo chifukwa chakulakwa ndiponso kunyada kwawo. Taona zimene zidawaonekera anthu olakwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وجحدوا بها واستيقنتها أنفسهم ظلما وعلوا فانظر كيف كان عاقبة المفسدين, باللغة نيانجا

﴿وجحدوا بها واستيقنتها أنفسهم ظلما وعلوا فانظر كيف كان عاقبة المفسدين﴾ [النَّمل: 14]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo adazitsutsa (zisonyezozo) mwachinyengo ndi modzikuza chikhalirecho mitima yawo idatsimikiza (kuti ndizoona zochokera kwa Allah); choncho, yang’ana adali bwanji malekezero a oononga
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek