Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 42 - النَّمل - Page - Juz 19
﴿فَلَمَّا جَآءَتۡ قِيلَ أَهَٰكَذَا عَرۡشُكِۖ قَالَتۡ كَأَنَّهُۥ هُوَۚ وَأُوتِينَا ٱلۡعِلۡمَ مِن قَبۡلِهَا وَكُنَّا مُسۡلِمِينَ ﴾
[النَّمل: 42]
﴿فلما جاءت قيل أهكذا عرشك قالت كأنه هو وأوتينا العلم من قبلها﴾ [النَّمل: 42]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho pamene (mfumukazi) idadza, kudanenedwa: “Kodi mpando wako wachifumu uli ngati uwu?” Idati: “Uli ngati umenewu, ndithu ndipo ife tidapatsidwa kuzindikira (za uneneri wanu) tisadaone chozizwitsa ichi; ndipo, ndithu tidadzipereka (kwa Allah).” |