Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 48 - النَّمل - Page - Juz 19
﴿وَكَانَ فِي ٱلۡمَدِينَةِ تِسۡعَةُ رَهۡطٖ يُفۡسِدُونَ فِي ٱلۡأَرۡضِ وَلَا يُصۡلِحُونَ ﴾
[النَّمل: 48]
﴿وكان في المدينة تسعة رهط يفسدون في الأرض ولا يصلحون﴾ [النَّمل: 48]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo m’mudzimo adalipo anthu asanu ndi anayi omwe amaononga pa dziko, ndipo samakonza (chilichonse koma kuchiononga) |