×

Ndithudi iwe siungathe kumupanga munthu wakufa kuti amve ndiponso siungathe kumupanga munthu 27:80 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Naml ⮕ (27:80) ayat 80 in Chichewa

27:80 Surah An-Naml ayat 80 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 80 - النَّمل - Page - Juz 20

﴿إِنَّكَ لَا تُسۡمِعُ ٱلۡمَوۡتَىٰ وَلَا تُسۡمِعُ ٱلصُّمَّ ٱلدُّعَآءَ إِذَا وَلَّوۡاْ مُدۡبِرِينَ ﴾
[النَّمل: 80]

Ndithudi iwe siungathe kumupanga munthu wakufa kuti amve ndiponso siungathe kumupanga munthu osamva kuti amve kuitana kwako pamene iye atembenuka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنك لا تسمع الموتى ولا تسمع الصم الدعاء إذا ولوا مدبرين, باللغة نيانجا

﴿إنك لا تسمع الموتى ولا تسمع الصم الدعاء إذا ولوا مدبرين﴾ [النَّمل: 80]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu iwe sungathe kuwachititsa kuti amve kuitana kwako akufa, ndiponso sungathe kuwachititsa kuti agonthi amve kuitanako, pamene akucheuka kutembenuza misana (osafuna kumva ulaliki wako)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek