×

Ndipo iwo akamva mawu oipa, salabadira zonenazo koma amati, “Ife tili ndi 28:55 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:55) ayat 55 in Chichewa

28:55 Surah Al-Qasas ayat 55 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 55 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَإِذَا سَمِعُواْ ٱللَّغۡوَ أَعۡرَضُواْ عَنۡهُ وَقَالُواْ لَنَآ أَعۡمَٰلُنَا وَلَكُمۡ أَعۡمَٰلُكُمۡ سَلَٰمٌ عَلَيۡكُمۡ لَا نَبۡتَغِي ٱلۡجَٰهِلِينَ ﴾
[القَصَص: 55]

Ndipo iwo akamva mawu oipa, salabadira zonenazo koma amati, “Ife tili ndi ntchito zathu ndipo nanunso muli ndi ntchito zanu. Mtendere ukhale kwa inu. Ife sitifuna kugwirizana ndi anthu osadziwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذا سمعوا اللغو أعرضوا عنه وقالوا لنا أعمالنا ولكم أعمالكم سلام عليكم, باللغة نيانجا

﴿وإذا سمعوا اللغو أعرضوا عنه وقالوا لنا أعمالنا ولكم أعمالكم سلام عليكم﴾ [القَصَص: 55]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo akamva zopanda pake amazipewa, ndipo amati (kwa achibwanawo): “Ife tili ndi zochita zathu inunso muli ndi zochita zanu, mtendere ukhale pa inu. Ife sitifuna (kutsutsana) ndi mbuli.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek