×

Ndipo anthu osakhulupirira amanena kwa anthu okhulupirira kuti, “Tsatirani njira yathu ndipo 29:12 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:12) ayat 12 in Chichewa

29:12 Surah Al-‘Ankabut ayat 12 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 12 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ لِلَّذِينَ ءَامَنُواْ ٱتَّبِعُواْ سَبِيلَنَا وَلۡنَحۡمِلۡ خَطَٰيَٰكُمۡ وَمَا هُم بِحَٰمِلِينَ مِنۡ خَطَٰيَٰهُم مِّن شَيۡءٍۖ إِنَّهُمۡ لَكَٰذِبُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 12]

Ndipo anthu osakhulupirira amanena kwa anthu okhulupirira kuti, “Tsatirani njira yathu ndipo ife tidzavomera chilango chifukwa cha kuchimwa kwanu. Iwo sadzavomera chilango china chilichonse m’malo mwawo. Ndithudi iwo ndi abodza

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وقال الذين كفروا للذين آمنوا اتبعوا سبيلنا ولنحمل خطاياكم وما هم بحاملين, باللغة نيانجا

﴿وقال الذين كفروا للذين آمنوا اتبعوا سبيلنا ولنحمل خطاياكم وما هم بحاملين﴾ [العَنكبُوت: 12]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene sadakhulupirire adanena kwa okhulupirira: “Tsatani njira yathu; (musatsate njira ya Muhammad). Ife tidzakusenzerani machimo anu (kuti chilichonse chisakupezeni). Koma sadzasenza chilichonse cha machimo awo, ndithu iwo ngabodza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek