×

Nena, “Yendani paliponse pa dziko lapansi ndipo muone mmene Mulungu adayambitsira chilengedwe. 29:20 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:20) ayat 20 in Chichewa

29:20 Surah Al-‘Ankabut ayat 20 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 20 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿قُلۡ سِيرُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ فَٱنظُرُواْ كَيۡفَ بَدَأَ ٱلۡخَلۡقَۚ ثُمَّ ٱللَّهُ يُنشِئُ ٱلنَّشۡأَةَ ٱلۡأٓخِرَةَۚ إِنَّ ٱللَّهَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[العَنكبُوت: 20]

Nena, “Yendani paliponse pa dziko lapansi ndipo muone mmene Mulungu adayambitsira chilengedwe. Kotero Mulungu adzalenga chilengedwe chinanso. Mulungu ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل سيروا في الأرض فانظروا كيف بدأ الخلق ثم الله ينشئ النشأة, باللغة نيانجا

﴿قل سيروا في الأرض فانظروا كيف بدأ الخلق ثم الله ينشئ النشأة﴾ [العَنكبُوت: 20]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Yendani pa dziko ndi kuona momwe Allah adayambitsira chilengedwe; kenako Allah adzaumba, kuumba kwina. Ndithu Allah Ndiwokhoza chilichonse.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek