×

Ndipo pamene Atumwi athu adadza kwa Abrahamu, ndi nkhani ya bwino, iwo 29:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:31) ayat 31 in Chichewa

29:31 Surah Al-‘Ankabut ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 31 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿وَلَمَّا جَآءَتۡ رُسُلُنَآ إِبۡرَٰهِيمَ بِٱلۡبُشۡرَىٰ قَالُوٓاْ إِنَّا مُهۡلِكُوٓاْ أَهۡلِ هَٰذِهِ ٱلۡقَرۡيَةِۖ إِنَّ أَهۡلَهَا كَانُواْ ظَٰلِمِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 31]

Ndipo pamene Atumwi athu adadza kwa Abrahamu, ndi nkhani ya bwino, iwo adati, “Ndithudi ife tidzaononga anthu a mu mzinda uno chifukwa anthu ake ndi osalungama.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولما جاءت رسلنا إبراهيم بالبشرى قالوا إنا مهلكو أهل هذه القرية إن, باللغة نيانجا

﴿ولما جاءت رسلنا إبراهيم بالبشرى قالوا إنا مهلكو أهل هذه القرية إن﴾ [العَنكبُوت: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene atumiki athu adamdzera Ibrahim ndi nkhani yabwino (yoti abereka Mneneri Ishaq), adanenanso: “Ndithu tiwaononga eni mudzi uwu (wa Sodom); ndithu iwowo ngochimwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek