×

Iye adati, “Ndithudi mu mzindamo muli Loti.” Iwo adati, “Ife tikudziwa amene 29:32 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:32) ayat 32 in Chichewa

29:32 Surah Al-‘Ankabut ayat 32 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 32 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿قَالَ إِنَّ فِيهَا لُوطٗاۚ قَالُواْ نَحۡنُ أَعۡلَمُ بِمَن فِيهَاۖ لَنُنَجِّيَنَّهُۥ وَأَهۡلَهُۥٓ إِلَّا ٱمۡرَأَتَهُۥ كَانَتۡ مِنَ ٱلۡغَٰبِرِينَ ﴾
[العَنكبُوت: 32]

Iye adati, “Ndithudi mu mzindamo muli Loti.” Iwo adati, “Ife tikudziwa amene ali m’menemo. Ndithudi ife tidzamupulumutsa iye ndi omutsatira ake onse kupatula mkazi wake. Iye adzakhala m’gulu la anthu otsalira.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال إن فيها لوطا قالوا نحن أعلم بمن فيها لننجينه وأهله إلا, باللغة نيانجا

﴿قال إن فيها لوطا قالوا نحن أعلم بمن فيها لننجينه وأهله إلا﴾ [العَنكبُوت: 32]

Khaled Ibrahim Betala
“(Mneneri Ibrahim) adati: “Koma mmenemo muli Luti.” Iwo adati: “Ife ndife odziwa kwambiri za omwe ali m’menemo; ndithu timpulumutsa iye ndi banja lake kupatula mkazi wake; iye ndi mmodzi wa otsalira (woonongeka).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek