×

Kotero tidalanga aliyense chifukwa cha machimo ake. Pakati pa iwo padali iwo 29:40 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:40) ayat 40 in Chichewa

29:40 Surah Al-‘Ankabut ayat 40 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 40 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿فَكُلًّا أَخَذۡنَا بِذَنۢبِهِۦۖ فَمِنۡهُم مَّنۡ أَرۡسَلۡنَا عَلَيۡهِ حَاصِبٗا وَمِنۡهُم مَّنۡ أَخَذَتۡهُ ٱلصَّيۡحَةُ وَمِنۡهُم مَّنۡ خَسَفۡنَا بِهِ ٱلۡأَرۡضَ وَمِنۡهُم مَّنۡ أَغۡرَقۡنَاۚ وَمَا كَانَ ٱللَّهُ لِيَظۡلِمَهُمۡ وَلَٰكِن كَانُوٓاْ أَنفُسَهُمۡ يَظۡلِمُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 40]

Kotero tidalanga aliyense chifukwa cha machimo ake. Pakati pa iwo padali iwo amene tidawatumizira mvula yamkuntho, ndipo pakati pawo padali iwo amene adavutika ndi mphenzi, ndipo pakati pawo padalinso iwo amene adamezedwa ndi nthaka ndipo padalinso iwo amene tidawamiza ndipo Mulungu sadalakwe ayi koma iwo ndiwo amene adalakwira mizimu yawo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فكلا أخذنا بذنبه فمنهم من أرسلنا عليه حاصبا ومنهم من أخذته الصيحة, باللغة نيانجا

﴿فكلا أخذنا بذنبه فمنهم من أرسلنا عليه حاصبا ومنهم من أخذته الصيحة﴾ [العَنكبُوت: 40]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho aliyense wa iwo tidamlanga ndi machimo ake. Ena a iwo tidawatumizira chimphepo chamiyala; ena a iwo udawaononga mkuwe; ena a iwo tidawadidimiza m’nthaka, ndipo ena a iwo tidawamiza (m’madzi). Si Allah amene adawachitira zoipa, koma adadzichitira okha zoipa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek