×

Kodi sizidakwanire kuti tavumbulutsa Buku lolemekezeka kwa iwe limene lili kuwerengedwa kwa 29:51 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:51) ayat 51 in Chichewa

29:51 Surah Al-‘Ankabut ayat 51 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 51 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿أَوَلَمۡ يَكۡفِهِمۡ أَنَّآ أَنزَلۡنَا عَلَيۡكَ ٱلۡكِتَٰبَ يُتۡلَىٰ عَلَيۡهِمۡۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَرَحۡمَةٗ وَذِكۡرَىٰ لِقَوۡمٖ يُؤۡمِنُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 51]

Kodi sizidakwanire kuti tavumbulutsa Buku lolemekezeka kwa iwe limene lili kuwerengedwa kwa iwo? Ndithudi m’Bukuli muli chifundo ndi chikumbutso kwa anthu okhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو لم يكفهم أنا أنـزلنا عليك الكتاب يتلى عليهم إن في ذلك, باللغة نيانجا

﴿أو لم يكفهم أنا أنـزلنا عليك الكتاب يتلى عليهم إن في ذلك﴾ [العَنكبُوت: 51]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi sizidawakwanire kuti takuvumbulutsira buku (ili) lomwe likuwerengedwa kwa iwo? Ndithu mmenemo muli chifundo ndi phunziro kwa anthu okhulupirira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek