×

Nena, “Mulungu ndi mboni yokwana pakati pa ine ndi inu. Iye amadziwa 29:52 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:52) ayat 52 in Chichewa

29:52 Surah Al-‘Ankabut ayat 52 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 52 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿قُلۡ كَفَىٰ بِٱللَّهِ بَيۡنِي وَبَيۡنَكُمۡ شَهِيدٗاۖ يَعۡلَمُ مَا فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِۗ وَٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ بِٱلۡبَٰطِلِ وَكَفَرُواْ بِٱللَّهِ أُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلۡخَٰسِرُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 52]

Nena, “Mulungu ndi mboni yokwana pakati pa ine ndi inu. Iye amadziwa chimene chili kumwamba ndi pa dziko lapansi.” Ndipo iwo amene amakhulupirira zabodza, ndiponso sakhulupirira mwa Mulungu, amenewa, ndi anthu olephera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل كفى بالله بيني وبينكم شهيدا يعلم ما في السموات والأرض والذين, باللغة نيانجا

﴿قل كفى بالله بيني وبينكم شهيدا يعلم ما في السموات والأرض والذين﴾ [العَنكبُوت: 52]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Allah akukwana kukhala mboni pakati panga ndi inu; akudziwa za kumwamba ndi zapansi ndipo amene akukhulupirira zachabe ndi kukana Allah, iwowo ndiwo otayika.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek