×

Ndithudi ngati iwe utawafunsa kuti kodi ndani amene adalenga kumwamba ndi dziko 29:61 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:61) ayat 61 in Chichewa

29:61 Surah Al-‘Ankabut ayat 61 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 61 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿وَلَئِن سَأَلۡتَهُم مَّنۡ خَلَقَ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضَ وَسَخَّرَ ٱلشَّمۡسَ وَٱلۡقَمَرَ لَيَقُولُنَّ ٱللَّهُۖ فَأَنَّىٰ يُؤۡفَكُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 61]

Ndithudi ngati iwe utawafunsa kuti kodi ndani amene adalenga kumwamba ndi dziko lapansi ndiponso amene adalamula dzuwa ndi mwezi kumvera malamulo ake? Ndithudi iwo adzayankha kuti ndi Mulungu. Nanga ndi chifukwa chiyani iwo amakana choonadi

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ولئن سألتهم من خلق السموات والأرض وسخر الشمس والقمر ليقولن الله فأنى, باللغة نيانجا

﴿ولئن سألتهم من خلق السموات والأرض وسخر الشمس والقمر ليقولن الله فأنى﴾ [العَنكبُوت: 61]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo ngati utawafunsa (kuti): “Kodi ndani adalenga thambo ndi nthaka, ndi kugonjetsa dzuwa ndi mwezi?” Ndithu anena: “Ndi Allah.” Nanga akutembenuzidwira kuti
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek