Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 65 - العَنكبُوت - Page - Juz 21
﴿فَإِذَا رَكِبُواْ فِي ٱلۡفُلۡكِ دَعَوُاْ ٱللَّهَ مُخۡلِصِينَ لَهُ ٱلدِّينَ فَلَمَّا نَجَّىٰهُمۡ إِلَى ٱلۡبَرِّ إِذَا هُمۡ يُشۡرِكُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 65]
﴿فإذا ركبوا في الفلك دعوا الله مخلصين له الدين فلما نجاهم إلى﴾ [العَنكبُوت: 65]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo akakwera m’chombo (ndi kukumana ndi zoopsa), amampempha Allah modzipereka ndikumuyeretsera pempho. Koma akawapulumutsa ndi kuwafikitsa ku ntunda, iwo amayambanso kumuphatikiza ndi mafano |