×

Ndipo moyo wa padziko lapansi siuli kanthu koma masewera ndi kongotayira nthawi. 29:64 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:64) ayat 64 in Chichewa

29:64 Surah Al-‘Ankabut ayat 64 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 64 - العَنكبُوت - Page - Juz 21

﴿وَمَا هَٰذِهِ ٱلۡحَيَوٰةُ ٱلدُّنۡيَآ إِلَّا لَهۡوٞ وَلَعِبٞۚ وَإِنَّ ٱلدَّارَ ٱلۡأٓخِرَةَ لَهِيَ ٱلۡحَيَوَانُۚ لَوۡ كَانُواْ يَعۡلَمُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 64]

Ndipo moyo wa padziko lapansi siuli kanthu koma masewera ndi kongotayira nthawi. Ukakhala moyo umene uli nkudza, umenewo ndiwo weniweni, iwo akadadziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما هذه الحياة الدنيا إلا لهو ولعب وإن الدار الآخرة لهي الحيوان, باللغة نيانجا

﴿وما هذه الحياة الدنيا إلا لهو ولعب وإن الدار الآخرة لهي الحيوان﴾ [العَنكبُوت: 64]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo moyo uwu wa pa dziko lapansi suli kanthu, koma chibwana ndi masewera. Ndipo ndithu nyumba ya tsiku la chimaliziro, ndiwo moyo weniweni, akadakhala akudziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek