×

Ndipo Ife tidamulamula munthu kuonetsa ubwino kwa makolo ake koma ngati iwo 29:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:8) ayat 8 in Chichewa

29:8 Surah Al-‘Ankabut ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 8 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿وَوَصَّيۡنَا ٱلۡإِنسَٰنَ بِوَٰلِدَيۡهِ حُسۡنٗاۖ وَإِن جَٰهَدَاكَ لِتُشۡرِكَ بِي مَا لَيۡسَ لَكَ بِهِۦ عِلۡمٞ فَلَا تُطِعۡهُمَآۚ إِلَيَّ مَرۡجِعُكُمۡ فَأُنَبِّئُكُم بِمَا كُنتُمۡ تَعۡمَلُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 8]

Ndipo Ife tidamulamula munthu kuonetsa ubwino kwa makolo ake koma ngati iwo akuuza kuti uzindiphatikiza Ine ndi ena ake amene iwe siuwazindikira, usawamvere ayi. Kwa Ine ndiko mudzabwerera ndipo ndidzakuuzani zimene munali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ووصينا الإنسان بوالديه حسنا وإن جاهداك لتشرك بي ما ليس لك به, باللغة نيانجا

﴿ووصينا الإنسان بوالديه حسنا وإن جاهداك لتشرك بي ما ليس لك به﴾ [العَنكبُوت: 8]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo tamulamula munthu kuchitira zabwino makolo ake. Koma ngati atakukakamiza (makolo ako) kuti undiphatikize Ine ndi (zinthu zina) zomwe iwe sukuzidziwa, usawamvere. Kwa Ine ndiko kobwerera kwanu, ndipo ndidzakuuzani zimene mumachita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek