×

Pamene iwe udanena kwa anthu okhulupirira: “Kodi simunakhutitsidwe pamene Ambuye anakuthandizani ndi 3:124 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:124) ayat 124 in Chichewa

3:124 Surah al-‘Imran ayat 124 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 124 - آل عِمران - Page - Juz 4

﴿إِذۡ تَقُولُ لِلۡمُؤۡمِنِينَ أَلَن يَكۡفِيَكُمۡ أَن يُمِدَّكُمۡ رَبُّكُم بِثَلَٰثَةِ ءَالَٰفٖ مِّنَ ٱلۡمَلَٰٓئِكَةِ مُنزَلِينَ ﴾
[آل عِمران: 124]

Pamene iwe udanena kwa anthu okhulupirira: “Kodi simunakhutitsidwe pamene Ambuye anakuthandizani ndi angelo zikwi zitatu amene adatsitsidwa kuchokera kumwamba kuti akuthandizeni?”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إذ تقول للمؤمنين ألن يكفيكم أن يمدكم ربكم بثلاثة آلاف من الملائكة, باللغة نيانجا

﴿إذ تقول للمؤمنين ألن يكفيكم أن يمدكم ربكم بثلاثة آلاف من الملائكة﴾ [آل عِمران: 124]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kumbukira) pamene umauza okhulupirira: “Kodi sizikukukwanirani pokuonjezerani Mbuye wanu zikwi zitatu za angelo otsitsidwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek