×

Ndiye amene wavumbulutsa kwa iwe Buku la choonadi, kutsimikiza mawu amene adaperekedwa 3:3 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:3) ayat 3 in Chichewa

3:3 Surah al-‘Imran ayat 3 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 3 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿نَزَّلَ عَلَيۡكَ ٱلۡكِتَٰبَ بِٱلۡحَقِّ مُصَدِّقٗا لِّمَا بَيۡنَ يَدَيۡهِ وَأَنزَلَ ٱلتَّوۡرَىٰةَ وَٱلۡإِنجِيلَ ﴾
[آل عِمران: 3]

Ndiye amene wavumbulutsa kwa iwe Buku la choonadi, kutsimikiza mawu amene adaperekedwa kale. Ndipo Iye anavumbulutsa Buku la chipangano chakale ndi Buku la chipangano chatsopano

❮ Previous Next ❯

ترجمة: نـزل عليك الكتاب بالحق مصدقا لما بين يديه وأنـزل التوراة والإنجيل, باللغة نيانجا

﴿نـزل عليك الكتاب بالحق مصدقا لما بين يديه وأنـزل التوراة والإنجيل﴾ [آل عِمران: 3]

Khaled Ibrahim Betala
“Wakuvumbulutsira buku mwachoonadi, lomwe likutsimikizira zomwe zidalipo patsogolo pake. Ndipo adavumbulutsa Taurat ndi Injil
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek