×

Ndipo Iye adzawapatsa malipiro abwino onse amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino 30:45 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Ar-Rum ⮕ (30:45) ayat 45 in Chichewa

30:45 Surah Ar-Rum ayat 45 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 45 - الرُّوم - Page - Juz 21

﴿لِيَجۡزِيَ ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ مِن فَضۡلِهِۦٓۚ إِنَّهُۥ لَا يُحِبُّ ٱلۡكَٰفِرِينَ ﴾
[الرُّوم: 45]

Ndipo Iye adzawapatsa malipiro abwino onse amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino kuchokera ku zokoma zake. Ndipo Iye sakonda anthu osakhulupirira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ليجزي الذين آمنوا وعملوا الصالحات من فضله إنه لا يحب الكافرين, باللغة نيانجا

﴿ليجزي الذين آمنوا وعملوا الصالحات من فضله إنه لا يحب الكافرين﴾ [الرُّوم: 45]

Khaled Ibrahim Betala
“Kuti awalipire zabwino Zake amene akhulupirira ndi kuchita zabwino. Ndithu Iye sakonda akafiri (osakhulupirira)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek