×

Kodiinusimuonammenezombozimayenderapanyanja mwachisomo cha Mulungu ndi mmene amakuonetserani inu zizindikiro zake? Ndithudi muli 31:31 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Luqman ⮕ (31:31) ayat 31 in Chichewa

31:31 Surah Luqman ayat 31 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Luqman ayat 31 - لُقمَان - Page - Juz 21

﴿أَلَمۡ تَرَ أَنَّ ٱلۡفُلۡكَ تَجۡرِي فِي ٱلۡبَحۡرِ بِنِعۡمَتِ ٱللَّهِ لِيُرِيَكُم مِّنۡ ءَايَٰتِهِۦٓۚ إِنَّ فِي ذَٰلِكَ لَأٓيَٰتٖ لِّكُلِّ صَبَّارٖ شَكُورٖ ﴾
[لُقمَان: 31]

Kodiinusimuonammenezombozimayenderapanyanja mwachisomo cha Mulungu ndi mmene amakuonetserani inu zizindikiro zake? Ndithudi muli chiphunzitso mu zimenezi kwa anthu olimbikira ndiponso kwa oyamika

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ألم تر أن الفلك تجري في البحر بنعمة الله ليريكم من آياته, باللغة نيانجا

﴿ألم تر أن الفلك تجري في البحر بنعمة الله ليريكم من آياته﴾ [لُقمَان: 31]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi suona kuti zombo zikuyenda pa nyanja mwachisomo cha Allah kuti akusonyezeni zisonyezo Zake (zamtendere Wake)? Ndithu M’zimenezo muli zisonyezo kwa yense wopirira, wothokoza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek