×

Oh iwe Mtumwi! Opa Mulungu ndipo usamvere zonena za anthu osakhulupirira ndi 33:1 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:1) ayat 1 in Chichewa

33:1 Surah Al-Ahzab ayat 1 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 1 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿يَٰٓأَيُّهَا ٱلنَّبِيُّ ٱتَّقِ ٱللَّهَ وَلَا تُطِعِ ٱلۡكَٰفِرِينَ وَٱلۡمُنَٰفِقِينَۚ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ عَلِيمًا حَكِيمٗا ﴾
[الأحزَاب: 1]

Oh iwe Mtumwi! Opa Mulungu ndipo usamvere zonena za anthu osakhulupirira ndi a chinyengo. Ndithudi Mulungu ndi wodziwa ndi waluntha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ياأيها النبي اتق الله ولا تطع الكافرين والمنافقين إن الله كان عليما, باللغة نيانجا

﴿ياأيها النبي اتق الله ولا تطع الكافرين والمنافقين إن الله كان عليما﴾ [الأحزَاب: 1]

Khaled Ibrahim Betala
“E iwe Mneneri! Muope Allah, ndipo usamvere osakhulupirira ndi achiphamaso. Ndithu Allah Ngodziwa kwambiri; Wanzeru zakuya (m’zoyankhula ndi m’zochita Zake)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek