Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 21 - الأحزَاب - Page - Juz 21
﴿لَّقَدۡ كَانَ لَكُمۡ فِي رَسُولِ ٱللَّهِ أُسۡوَةٌ حَسَنَةٞ لِّمَن كَانَ يَرۡجُواْ ٱللَّهَ وَٱلۡيَوۡمَ ٱلۡأٓخِرَ وَذَكَرَ ٱللَّهَ كَثِيرٗا ﴾
[الأحزَاب: 21]
﴿لقد كان لكم في رسول الله أسوة حسنة لمن كان يرجو الله﴾ [الأحزَاب: 21]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithu muli nacho chitsanzo chabwino mwa Mthenga wa Allah (m’kudzipereka kwake ndi khama lake pa njira ya Allah, ndi kupirira kwake ndi masautso) kwa yemwe akuopa Allah ndi tsiku lachimaliziro, namatchula Allah kwambiri |