×

Iwo akuganiza kuti owathandiza awo alipo ndipo ngati iwo akadabweranso iwo akadafuna 33:20 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:20) ayat 20 in Chichewa

33:20 Surah Al-Ahzab ayat 20 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 20 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿يَحۡسَبُونَ ٱلۡأَحۡزَابَ لَمۡ يَذۡهَبُواْۖ وَإِن يَأۡتِ ٱلۡأَحۡزَابُ يَوَدُّواْ لَوۡ أَنَّهُم بَادُونَ فِي ٱلۡأَعۡرَابِ يَسۡـَٔلُونَ عَنۡ أَنۢبَآئِكُمۡۖ وَلَوۡ كَانُواْ فِيكُم مَّا قَٰتَلُوٓاْ إِلَّا قَلِيلٗا ﴾
[الأحزَاب: 20]

Iwo akuganiza kuti owathandiza awo alipo ndipo ngati iwo akadabweranso iwo akadafuna akadakhala ali m’chipululu pamodzi ndi anthu okhala m’chipululu ndi kufunsa nkhani zokhudza iwe kuchokera kutali. Ndipo iwo akadakhala pakati panu, akadamenya nkhondo pang’ono

❮ Previous Next ❯

ترجمة: يحسبون الأحزاب لم يذهبوا وإن يأت الأحزاب يودوا لو أنهم بادون في, باللغة نيانجا

﴿يحسبون الأحزاب لم يذهبوا وإن يأت الأحزاب يودوا لو أنهم بادون في﴾ [الأحزَاب: 20]

Khaled Ibrahim Betala
“(Kufikira tsopano chifukwa cha mantha awo) akuganiza kuti magulu a nkhondo (adani) sadapitebe; ndipo magulu amenewo akadadzanso, akadalakalaka akadakhala kuchipululu pamodzi ndi arabu a kuchimidzi ndi kuti azikangofunsa za nkhani zanu. Akadakhala pamodzi ndi inu sadakamenyana (ndi adani) koma pang’ono pokha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek