×

Ndipo iwo amene amayankhula zinthu zoipa zokhudza anthu a amuna okhulupirira ndi 33:58 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:58) ayat 58 in Chichewa

33:58 Surah Al-Ahzab ayat 58 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 58 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿وَٱلَّذِينَ يُؤۡذُونَ ٱلۡمُؤۡمِنِينَ وَٱلۡمُؤۡمِنَٰتِ بِغَيۡرِ مَا ٱكۡتَسَبُواْ فَقَدِ ٱحۡتَمَلُواْ بُهۡتَٰنٗا وَإِثۡمٗا مُّبِينٗا ﴾
[الأحزَاب: 58]

Ndipo iwo amene amayankhula zinthu zoipa zokhudza anthu a amuna okhulupirira ndi anthu a akazi okhulupirira, pamene iwo sadalakwe, iwowo ali pamlandu wonamizira ndi wochita tchimo looneka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين يؤذون المؤمنين والمؤمنات بغير ما اكتسبوا فقد احتملوا بهتانا وإثما مبينا, باللغة نيانجا

﴿والذين يؤذون المؤمنين والمؤمنات بغير ما اكتسبوا فقد احتملوا بهتانا وإثما مبينا﴾ [الأحزَاب: 58]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akuvutitsa okhulupirira aamuna ndi okhulupirira aakazi popanda kuchimwa kulikonse, ndithu asenza chinyengo ndi tchimo loonekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek