×

Ndithudi Ife tidapereka udindo ndi chikhulupiriro kumwamba, pa dziko ndi pa mapiri 33:72 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:72) ayat 72 in Chichewa

33:72 Surah Al-Ahzab ayat 72 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 72 - الأحزَاب - Page - Juz 22

﴿إِنَّا عَرَضۡنَا ٱلۡأَمَانَةَ عَلَى ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَٱلۡجِبَالِ فَأَبَيۡنَ أَن يَحۡمِلۡنَهَا وَأَشۡفَقۡنَ مِنۡهَا وَحَمَلَهَا ٱلۡإِنسَٰنُۖ إِنَّهُۥ كَانَ ظَلُومٗا جَهُولٗا ﴾
[الأحزَاب: 72]

Ndithudi Ife tidapereka udindo ndi chikhulupiriro kumwamba, pa dziko ndi pa mapiri koma zonse zidakana kulandira ndipo adauopa. Koma munthu adauvomera. Ndithudi iye ndi wosalungama ndiponso mbuli

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنا عرضنا الأمانة على السموات والأرض والجبال فأبين أن يحملنها وأشفقن منها, باللغة نيانجا

﴿إنا عرضنا الأمانة على السموات والأرض والجبال فأبين أن يحملنها وأشفقن منها﴾ [الأحزَاب: 72]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu Ife tidapereka udindo (otsatira malamulo) ku thambo ndi nthaka ndi mapiri; koma zidakana kuwusenza (udindowo); ndipo zidauopa. Koma munthu adawusenza; ndithu iye ngwachinyengo kwambiri ndiponso mbuli
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek