Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 17 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿ذَٰلِكَ جَزَيۡنَٰهُم بِمَا كَفَرُواْۖ وَهَلۡ نُجَٰزِيٓ إِلَّا ٱلۡكَفُورَ ﴾
[سَبإ: 17]
﴿ذلك جزيناهم بما كفروا وهل نجازي إلا الكفور﴾ [سَبإ: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Amenewo ndiwo malipiro tidawalipira chifukwa cha kusathokoza kwawo (mtendere wa Allah). Ndipo Ife sitilipira zoterezi koma kwa okhawo osathokoza |