Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 12 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿وَمَا يَسۡتَوِي ٱلۡبَحۡرَانِ هَٰذَا عَذۡبٞ فُرَاتٞ سَآئِغٞ شَرَابُهُۥ وَهَٰذَا مِلۡحٌ أُجَاجٞۖ وَمِن كُلّٖ تَأۡكُلُونَ لَحۡمٗا طَرِيّٗا وَتَسۡتَخۡرِجُونَ حِلۡيَةٗ تَلۡبَسُونَهَاۖ وَتَرَى ٱلۡفُلۡكَ فِيهِ مَوَاخِرَ لِتَبۡتَغُواْ مِن فَضۡلِهِۦ وَلَعَلَّكُمۡ تَشۡكُرُونَ ﴾
[فَاطِر: 12]
﴿وما يستوي البحران هذا عذب فرات سائغ شرابه وهذا ملح أجاج ومن﴾ [فَاطِر: 12]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo nyanja ziwiri (ya madzi ozizira ndi yamadzi amchere) sizili zofanana, iyi yamadzi okoma, ozuna, ndi omweka bwino kamwedwe kake; ndi iyi (ya madzi) amchere owawa. Ndipo kuchokera m’zonsezi, mumadya nyama yamatumbi (nsomba zaziwisi). Ndipo mumatulutsa zodzikongoletsera (zimene) mumazivala; ndipo m’menemo ukuona zombo zikung’amba madzi kuti mufunefune ubwino Wake (wa Allah) ndi kutinso inu muthokoze |