×

Kodi iwo sadayende padziko lapansi ndi kuona zimene zidawachitikira anthu amene adalipo 35:44 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:44) ayat 44 in Chichewa

35:44 Surah FaTir ayat 44 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 44 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿أَوَلَمۡ يَسِيرُواْ فِي ٱلۡأَرۡضِ فَيَنظُرُواْ كَيۡفَ كَانَ عَٰقِبَةُ ٱلَّذِينَ مِن قَبۡلِهِمۡ وَكَانُوٓاْ أَشَدَّ مِنۡهُمۡ قُوَّةٗۚ وَمَا كَانَ ٱللَّهُ لِيُعۡجِزَهُۥ مِن شَيۡءٖ فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَلَا فِي ٱلۡأَرۡضِۚ إِنَّهُۥ كَانَ عَلِيمٗا قَدِيرٗا ﴾
[فَاطِر: 44]

Kodi iwo sadayende padziko lapansi ndi kuona zimene zidawachitikira anthu amene adalipo kale pamene mitundu ya anthuwo idali yamphamvu kuposa iwo? Kulibe chinthu kumwamba kapena padziko lapansi chimene chingakhumudwitse Mulungu chifukwa Iye amadziwa chilichonse ndipo ndi mwini mphamvu zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو لم يسيروا في الأرض فينظروا كيف كان عاقبة الذين من قبلهم, باللغة نيانجا

﴿أو لم يسيروا في الأرض فينظروا كيف كان عاقبة الذين من قبلهم﴾ [فَاطِر: 44]

Khaled Ibrahim Betala
“Kodi sadayende pa dziko nkuona momwe adalili mathero a omwe adali patsogolo pawo? Ndipo adali anyonga kwambiri kuposa iwo? Ndipo palibe chinthu chonkanika Allah kumwamba ndi pansi. Ndithudi Iye Ngodziwa kwabasi Wokhoza
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek