Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 45 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿وَلَوۡ يُؤَاخِذُ ٱللَّهُ ٱلنَّاسَ بِمَا كَسَبُواْ مَا تَرَكَ عَلَىٰ ظَهۡرِهَا مِن دَآبَّةٖ وَلَٰكِن يُؤَخِّرُهُمۡ إِلَىٰٓ أَجَلٖ مُّسَمّٗىۖ فَإِذَا جَآءَ أَجَلُهُمۡ فَإِنَّ ٱللَّهَ كَانَ بِعِبَادِهِۦ بَصِيرَۢا ﴾
[فَاطِر: 45]
﴿ولو يؤاخذ الله الناس بما كسبوا ما ترك على ظهرها من دابة﴾ [فَاطِر: 45]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo Allah akadamalanga anthu chifukwa cha zomwe alakwa, sakadasiya pamwamba pake (pa nthaka) chamoyo chilichonse; koma Iye amawalekelera mpaka nthawi yomwe adaiikayo. Choncho nthawi yawo ikadzawadzera, (pompo adzalangidwa). Ndithu Allah akuwadziwa bwino akapolo Ake |