Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 25 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿مَا لَكُمۡ لَا تَنَاصَرُونَ ﴾
[الصَّافَات: 25]
﴿ما لكم لا تناصرون﴾ [الصَّافَات: 25]
Khaled Ibrahim Betala ““Kodi nchifukwa ninji inu (opembedza mafano) simukupulumutsana (monga mumanenera pa dziko lapansi kuti mudzapulumutsana)?” |