×

Khala wopirira pa zimene ali kunena ndipo uzikumbukira kapolo wathu Davide, munthu 38:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:17) ayat 17 in Chichewa

38:17 Surah sad ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 17 - صٓ - Page - Juz 23

﴿ٱصۡبِرۡ عَلَىٰ مَا يَقُولُونَ وَٱذۡكُرۡ عَبۡدَنَا دَاوُۥدَ ذَا ٱلۡأَيۡدِۖ إِنَّهُۥٓ أَوَّابٌ ﴾
[صٓ: 17]

Khala wopirira pa zimene ali kunena ndipo uzikumbukira kapolo wathu Davide, munthu wamphamvu. Ndithudi iye anali kulapa nthawi zonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: اصبر على ما يقولون واذكر عبدنا داود ذا الأيد إنه أواب, باللغة نيانجا

﴿اصبر على ما يقولون واذكر عبدنا داود ذا الأيد إنه أواب﴾ [صٓ: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Pirira (iwe Mtumiki) ku zimene akunena (kwa iwe), ndipo kumbuka kapolo wathu Daud, wamphamvu (pa chipembedzo ndi za m’dziko lapansi). Ndithu iye ngotembenukira kwa Allah kwambiri
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek