×

“Ndithudi uyu ndi m’bale wanga ndipo ali ndi nkhosa makumi asanu ndi 38:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:23) ayat 23 in Chichewa

38:23 Surah sad ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 23 - صٓ - Page - Juz 23

﴿إِنَّ هَٰذَآ أَخِي لَهُۥ تِسۡعٞ وَتِسۡعُونَ نَعۡجَةٗ وَلِيَ نَعۡجَةٞ وَٰحِدَةٞ فَقَالَ أَكۡفِلۡنِيهَا وَعَزَّنِي فِي ٱلۡخِطَابِ ﴾
[صٓ: 23]

“Ndithudi uyu ndi m’bale wanga ndipo ali ndi nkhosa makumi asanu ndi anayi kudza mphambu zisanu ndi zinayi pamene ine ndili ndi nkhosa imodzi yokha basi. Komabe iye akuti, ‘Undipatse ine nkhosayo’ ndipo iye adandipambana mu zonena zake.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن هذا أخي له تسع وتسعون نعجة ولي نعجة واحدة فقال أكفلنيها, باللغة نيانجا

﴿إن هذا أخي له تسع وتسعون نعجة ولي نعجة واحدة فقال أكفلنيها﴾ [صٓ: 23]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndithu uyu m’bale wanga ali ndi nkhosa makumi asanu ndi anayi mphambu zisanu ndi zinayi , pomwe ine ndili ndi imodzi.” Ndipo akuti: “Ndipatse nkhosa imodziyo kuti ndizikusungira.” Ndipo wandiposa pakuyankhula
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek