×

Iye adati, “Ndithudi iye wakulakwira kwambiri pokupempha kuti nkhosa yako imodzi yokha 38:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah sad ⮕ (38:24) ayat 24 in Chichewa

38:24 Surah sad ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah sad ayat 24 - صٓ - Page - Juz 23

﴿قَالَ لَقَدۡ ظَلَمَكَ بِسُؤَالِ نَعۡجَتِكَ إِلَىٰ نِعَاجِهِۦۖ وَإِنَّ كَثِيرٗا مِّنَ ٱلۡخُلَطَآءِ لَيَبۡغِي بَعۡضُهُمۡ عَلَىٰ بَعۡضٍ إِلَّا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ وَقَلِيلٞ مَّا هُمۡۗ وَظَنَّ دَاوُۥدُ أَنَّمَا فَتَنَّٰهُ فَٱسۡتَغۡفَرَ رَبَّهُۥ وَخَرَّۤ رَاكِعٗاۤ وَأَنَابَ۩ ﴾
[صٓ: 24]

Iye adati, “Ndithudi iye wakulakwira kwambiri pokupempha kuti nkhosa yako imodzi yokha iperekedwe kwa iye kuonjezera pa zimene ali nazo.” Ndithudi anthu ambiri ochitira pamodzi malonda ndi amene akulakwirana wina ndi mnzake. Koma izi sizichitika ndi anthu amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino ndipo anthu otere ndi ochepa. Ndipo Davide adazindikira kuti Ife tidamuyesa iye ndipo adapempha chikhululukiro kwa Ambuye wake ndipo iye adagwa nagunditsa mphumi yake pansi ndi kudza molapa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال لقد ظلمك بسؤال نعجتك إلى نعاجه وإن كثيرا من الخلطاء ليبغي, باللغة نيانجا

﴿قال لقد ظلمك بسؤال نعجتك إلى نعاجه وإن كثيرا من الخلطاء ليبغي﴾ [صٓ: 24]

Khaled Ibrahim Betala
“(Daud) adati: “Zoona, wakuchitira zosalungama pokupempha nkhosa yako imodzi kuti aiphatikize ndi nkhosa zake. Ndithu ambiri mwa ophatikizana nawo zinthu, ena amachenjelera ena kupatula amene akhulupirira ndi kumachita zabwino; ndipo iwo ngochepa.” Basi pamenepo Daud adaona kuti tamuyesa mayeso (ndipo sadapambane). Choncho adapempha chikhululuko kwa Mbuye wake; adagwa ndi kulambira ndi kubwerera kwa Mbuye wake
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek